Add parallel Print Page Options

52 Kodi analipo mneneri amene makolo anu sanamuzunze? Iwo anapha ngakhale amene ananeneratu za kubwera kwa Wolungamayo. Ndipo tsopano inu munamupereka ndi kumupha Iye.

Read full chapter

52 Was there ever a prophet your ancestors did not persecute?(A) They even killed those who predicted the coming of the Righteous One. And now you have betrayed and murdered him(B)

Read full chapter